Perspectives on
music & culture
Insights, stories, and analysis from the frontlines of music distribution in Malawi and across Africa.

2024 Annual Newsletter
Empowering Malawian artists through innovative distribution, education, and community building – reflecting on a year of growth, digital transformation, and musical excellence COO’s Remarks “2024 has been such a pivotal year for Newwave!

Copyright Fundamentals in Malawi
Understanding the basics of copyright is essential for creators in Malawi

Nsanamira za mphamvu ya umwini mu Malawi
Kumvetsetsa/Kuzindikira nsanamira za mphamvu ya umwini ndikofunikira kwambiri kwa anthu a luso muno mu Malawi.

Copyright Registration in Malawi
Registering copyright in Malawi is not mandatory, but it offers several benefits

Kulembetsa mphamvu ya umwini
Kulembetsa mphamvu yanu ya umwini ku Malawi kuno si kokakamiza, koma kumapindulitsa.

Copyright Infringement and Enforcement
Protecting copyright in Malawi involves identifying and responding to infringement

Kunyozera/kuswa lamulo la mphamvu ya umwini komanso kagwiritsidwe ntchito
Kuteteza mphamvu ya umwini muno mu Malawi kumaphatikizapo kuzindikira ndi kuchitapo kanthu pamene lamulo la mphamvu ya umwini laswedwa.

Introduction to Music Distribution
Music distribution is a crucial aspect of a musician's career in Malawi, as it directly impacts their reach and revenue.

Kuyamba Kwa Gawo lofalitsa nyimbo
Gawo lofalitsa nyimbo ndilofunikira kwambiri ku ntchito ya oyimba muno mu Malawi, chifukwa imakhudza mulingo wa anthu amene angafikilidwe ndi phindu la ndalama limene lingapezeke.